Numeri 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anati: “Paja Yehova anakulamulani inu mbuyathu, kuti mugawire dzikoli ana a Isiraeli monga cholowa chawo, mwa kuchita maere.+ Yehova anakulamulaninso kuti cholowa cha m’bale wathu Tselofekadi muchipereke kwa ana ake aakazi.+
2 Iwo anati: “Paja Yehova anakulamulani inu mbuyathu, kuti mugawire dzikoli ana a Isiraeli monga cholowa chawo, mwa kuchita maere.+ Yehova anakulamulaninso kuti cholowa cha m’bale wathu Tselofekadi muchipereke kwa ana ake aakazi.+