Deuteronomo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la Chilamulo ichi, kuchokera mʼbuku limene* Alevi omwe ndi ansembe amasunga.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:18 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 205/1/1995, ptsa. 12-13
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la Chilamulo ichi, kuchokera mʼbuku limene* Alevi omwe ndi ansembe amasunga.+