Deuteronomo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:10 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, ptsa. 4-5
10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+