Oweruza 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamapeto pake, Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli+ ndipo anati: “Popeza mtundu umenewu waphwanya pangano langa+ limene ndinalamula makolo awo kuti alisunge, ndipo sanandimvere,+
20 Pamapeto pake, Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli+ ndipo anati: “Popeza mtundu umenewu waphwanya pangano langa+ limene ndinalamula makolo awo kuti alisunge, ndipo sanandimvere,+