Oweruza 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero mkwiyo wa Yehova unayakira+ Isiraeli ndipo anati: “Popeza mtundu umenewu waphwanya pangano langa+ limene ndinalamula makolo awo kuti alisunge, ndipo sanamvere mawu anga,+
20 Chotero mkwiyo wa Yehova unayakira+ Isiraeli ndipo anati: “Popeza mtundu umenewu waphwanya pangano langa+ limene ndinalamula makolo awo kuti alisunge, ndipo sanamvere mawu anga,+