Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndileke tsopano kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize,+ koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+

  • Deuteronomo 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti adzapatutsa ana ako aamuna kuti asanditsatire ndipo adzatumikira ndithu milungu ina.+ Pamenepo mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo adzakuwonongani ndithu mofulumira.+

  • Deuteronomo 32:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+

      Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+

      Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+

      Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+

  • Oweruza 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+

  • Salimo 106:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Mkwiyo wa Yehova unayamba kuyakira anthu ake,+

      Ndipo iye ananyansidwa ndi cholowa chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena