1 Mbiri 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkuwoloka Yorodano kupita kukakumana nawo ndipo anakonzekera kumenya nkhondo. Davide anakonzekera kuti amenyane ndi Asiriya ndipo Asiriyawo anayamba kumenyana naye.+
17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkuwoloka Yorodano kupita kukakumana nawo ndipo anakonzekera kumenya nkhondo. Davide anakonzekera kuti amenyane ndi Asiriya ndipo Asiriyawo anayamba kumenyana naye.+