1 Mbiri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yowabu anapereka kwa Davide chiwerengero cha anthu amene anawerengedwa. Amuna onse a mafuko a Isiraeli okhala ndi lupanga analipo 1,100,000 ndipo amuna a fuko la Yuda okhala ndi lupanga, analipo 470,000.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 5
5 Yowabu anapereka kwa Davide chiwerengero cha anthu amene anawerengedwa. Amuna onse a mafuko a Isiraeli okhala ndi lupanga analipo 1,100,000 ndipo amuna a fuko la Yuda okhala ndi lupanga, analipo 470,000.+