1 Mbiri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, Yowabu anapereka chiwerengero chonse cha anthu kwa Davide. Aisiraeli onse analipo 1,100,000, amuna ogwira lupanga,+ ndipo amuna a Yuda ogwira lupanga analipo 470,000. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 5
5 Atafika kumeneko, Yowabu anapereka chiwerengero chonse cha anthu kwa Davide. Aisiraeli onse analipo 1,100,000, amuna ogwira lupanga,+ ndipo amuna a Yuda ogwira lupanga analipo 470,000.