1 Mbiri 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli, moti anthu 70,000 anafa mu Isiraeli.+