1 Mbiri 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli, moti mu Isiraeli munafa anthu 70,000.+