2 Mbiri 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100+ aja mikondo, zishango zingʼonozingʼono* ndiponso zishango zozungulira zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali mʼnyumba ya Mulungu woona.+
9 Kenako wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100+ aja mikondo, zishango zingʼonozingʼono* ndiponso zishango zozungulira zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali mʼnyumba ya Mulungu woona.+