2 Mbiri 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera apo, wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100 aja+ mikondo, zishango ndi zishango zozungulira+ zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali m’nyumba ya Mulungu woona.+
9 Kuwonjezera apo, wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100 aja+ mikondo, zishango ndi zishango zozungulira+ zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali m’nyumba ya Mulungu woona.+