2 Mbiri 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hezekiya anatumiza uthenga kwa Aisiraeli+ ndi Ayuda onse ndipo analembera makalata anthu a ku Efuraimu ndi ku Manase+ kuti abwere kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu kudzachitira Pasika Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
30 Hezekiya anatumiza uthenga kwa Aisiraeli+ ndi Ayuda onse ndipo analembera makalata anthu a ku Efuraimu ndi ku Manase+ kuti abwere kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu kudzachitira Pasika Yehova Mulungu wa Isiraeli.+