Nehemiya 7:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ansembe anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi+ ndiponso ana a Barizilai amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ wa ku Giliyadi nʼkuyamba kutchedwa ndi dzina lawo.
63 Ansembe anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi+ ndiponso ana a Barizilai amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ wa ku Giliyadi nʼkuyamba kutchedwa ndi dzina lawo.