Salimo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu amene amafunitsitsa kulambira milungu ina amachulukitsa chisoni chawo.+ Ine sindidzapereka nsembe zachakumwa za magazi kwa milungu ina,Ndipo milomo yanga sidzatchula mayina awo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, ptsa. 27-28
4 Anthu amene amafunitsitsa kulambira milungu ina amachulukitsa chisoni chawo.+ Ine sindidzapereka nsembe zachakumwa za magazi kwa milungu ina,Ndipo milomo yanga sidzatchula mayina awo.+