Salimo 119:125 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Ine ndine mtumiki wanu. Ndithandizeni kukhala wozindikira,+Kuti ndidziwe zikumbutso zanu.