Salimo 119:125 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Ine ndine mtumiki wanu.+ Ndithandizeni kukhala wozindikira,+Kuti ndidziwe zikumbutso zanu.+