2 Mbiri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+ Salimo 119:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+ 2 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Uziganizira zimene ndikukuuzazi nthawi zonse. Ndithudi, Ambuye adzakuthandiza kuzindikira+ zinthu zonse. Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+
10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+
34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+
7 Uziganizira zimene ndikukuuzazi nthawi zonse. Ndithudi, Ambuye adzakuthandiza kuzindikira+ zinthu zonse.
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+