Numeri 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+ 2 Samueli 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuyambira kale+ pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa Isiraeli.’”
17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+
2 Kuyambira kale+ pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa Isiraeli.’”