Salimo 116:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova,+Inetu ndine mtumiki wanu.+Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi.+Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+ Aroma 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+
16 Inu Yehova,+Inetu ndine mtumiki wanu.+Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi.+Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+
22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+