Salimo 138:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzawerama nditayangʼana kukachisi wanu woyera,*+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu+Chifukwa cha kukhulupirika kwanu ndiponso chikondi chanu chokhulupirika. Chifukwa mwasonyeza kuti dzina lanu komanso malonjezo anu ndi apamwamba kuposa china chilichonse.* Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 138:2 Nsanja ya Olonda,10/1/2006, tsa. 199/1/2006, tsa. 163/15/1987, tsa. 29
2 Ndidzawerama nditayangʼana kukachisi wanu woyera,*+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu+Chifukwa cha kukhulupirika kwanu ndiponso chikondi chanu chokhulupirika. Chifukwa mwasonyeza kuti dzina lanu komanso malonjezo anu ndi apamwamba kuposa china chilichonse.*