2 Ndidzawerama nditayang’ana kukachisi wanu woyera,+
Ndipo ndidzatamanda dzina lanu+
Chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha+ ndi choonadi chanu.+
Pakuti malonjezo+ amene munawachita m’dzina lanu ndi aakulu ndithu. Koma kukwaniritsidwa kwa malonjezowo n’kwakukulu koposa.+