Salimo 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu,+ ndidzatamanda mawu ake.Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Yehova, ndidzatamanda mawu ake.+ Yesaya 42:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa cha chilungamo chake,+ Yehova walemekeza ndi kukweza malamulo ake mokondwera.+ Aheberi 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.
10 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu,+ ndidzatamanda mawu ake.Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Yehova, ndidzatamanda mawu ake.+
17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.