Yesaya 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Madzi onse a ku Dimoni adzaza magazi,Ndipo Mulungu adzamʼbweretsera Dimoni masoka ambiri, Adzatumiza mikango kwa anthu a ku Mowabu amene adzathaweKomanso kwa anthu otsala mʼdzikolo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:9 Yesaya 1, tsa. 193
9 Madzi onse a ku Dimoni adzaza magazi,Ndipo Mulungu adzamʼbweretsera Dimoni masoka ambiri, Adzatumiza mikango kwa anthu a ku Mowabu amene adzathaweKomanso kwa anthu otsala mʼdzikolo.+