Yesaya 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa m’madzi onse a ku Dimoni mwadzaza magazi. Dimoni ndidzam’bweretsera zinthu zinanso, monga mikango yoti idye anthu othawa ku Mowabu ndi anthu otsala panthaka yawo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:9 Yesaya 1, tsa. 193
9 chifukwa m’madzi onse a ku Dimoni mwadzaza magazi. Dimoni ndidzam’bweretsera zinthu zinanso, monga mikango yoti idye anthu othawa ku Mowabu ndi anthu otsala panthaka yawo.+