Levitiko 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu, ndi kuchepetsa chiwerengero chanu, moti m’misewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+ 2 Mafumu 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo. Yeremiya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ndidzawagwetsera masoka a mitundu inayi,’+ watero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, zolengedwa zouluka zam’mlengalenga+ ndi zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga. Amosi 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+
22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu, ndi kuchepetsa chiwerengero chanu, moti m’misewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+
25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo.
3 “‘Ndidzawagwetsera masoka a mitundu inayi,’+ watero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, zolengedwa zouluka zam’mlengalenga+ ndi zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.
19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+