Yesaya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku limenelo mizinda yake yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri idzakhala ngati malo amene angosiyidwa mʼnkhalango.+Idzakhala ngati nthambi imene anthu anangoisiya chifukwa cha Aisiraeli,Ndipo idzakhala chipululu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:9 Yesaya 1, ptsa. 196-197
9 Tsiku limenelo mizinda yake yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri idzakhala ngati malo amene angosiyidwa mʼnkhalango.+Idzakhala ngati nthambi imene anthu anangoisiya chifukwa cha Aisiraeli,Ndipo idzakhala chipululu.