Yesaya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’tsiku limenelo mizinda yake yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri idzakhala ngati malo amene angosiyidwa m’nkhalango. Idzakhala ngati nthambi imene anthu angoisiya chifukwa cha ana a Isiraeli, ndipo idzakhala bwinja.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:9 Yesaya 1, ptsa. 196-197
9 M’tsiku limenelo mizinda yake yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri idzakhala ngati malo amene angosiyidwa m’nkhalango. Idzakhala ngati nthambi imene anthu angoisiya chifukwa cha ana a Isiraeli, ndipo idzakhala bwinja.+