Yesaya 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zomera zamʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo, kumene mtsinje wa Nailo wakathera,Komanso malo onse amʼmphepete mwa mtsinjewo odzalidwa mbewu,+ adzauma.+ Zomera zamʼmphepete mwa mtsinjewo zidzauma ndipo zidzauluzika ndi mphepo.
7 Zomera zamʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo, kumene mtsinje wa Nailo wakathera,Komanso malo onse amʼmphepete mwa mtsinjewo odzalidwa mbewu,+ adzauma.+ Zomera zamʼmphepete mwa mtsinjewo zidzauma ndipo zidzauluzika ndi mphepo.