Yesaya 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madambo a m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, malo othera mtsinje wa Nailo, ndi malo onse obzala mbewu m’mphepete mwa mtsinjewo, adzauma.+ Zomera za m’mphepete mwa mtsinjewo zidzauma ndipo zidzauluzika ndi mphepo.
7 Madambo a m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, malo othera mtsinje wa Nailo, ndi malo onse obzala mbewu m’mphepete mwa mtsinjewo, adzauma.+ Zomera za m’mphepete mwa mtsinjewo zidzauma ndipo zidzauluzika ndi mphepo.