Yesaya 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:11 Yesaya 1, ptsa. 202-203
11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”?