Yesaya 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye kodi anthu ako anzeruwo ali kuti?+ Akuuze, ngati akudziwa zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakonza zokhudza Iguputo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Yesaya 1, ptsa. 202-203
12 Ndiye kodi anthu ako anzeruwo ali kuti?+ Akuuze, ngati akudziwa zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakonza zokhudza Iguputo.