Yesaya 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi anthu ako anzeruwo ali kuti?+ Ngati akudziwa, akuuze zimene Yehova wa makamu wakonza zokhudza Iguputo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Yesaya 1, ptsa. 202-203
12 Kodi anthu ako anzeruwo ali kuti?+ Ngati akudziwa, akuuze zimene Yehova wa makamu wakonza zokhudza Iguputo.+