Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo.

  • 1 Mafumu 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Nzeru za Solomo zinaposa+ nzeru za anthu onse a Kum’mawa+ ndi nzeru zonse za ku Iguputo.+

  • Mlaliki 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zonsezi ndinazifufuza mwanzeru ndipo ndinati: “Ndidzakhala wanzeru.” Koma nzeruzo zinatalikirana nane.+

  • Machitidwe 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena