Deuteronomo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Zinthu zobisika+ ndi za Yehova Mulungu wathu, koma zinthu zoululidwa+ ndi zathu ndi ana athu mpaka kalekale, kuti titsatire mawu onse a chilamulo ichi.+ Yobu 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma kodi nzeru zingapezeke kuti?+Ndipo kumvetsa zinthu, malo ake ali kuti? Salimo 119:114 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 114 Inu ndinu malo anga obisalamo ndi chishango changa,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+
29 “Zinthu zobisika+ ndi za Yehova Mulungu wathu, koma zinthu zoululidwa+ ndi zathu ndi ana athu mpaka kalekale, kuti titsatire mawu onse a chilamulo ichi.+