Yesaya 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzalanga Iguputo.+ Adzamulanga kenako nʼkumuchiritsa. Iwo adzabwerera kwa Yehova ndipo iye adzamva kuchonderera kwawo nʼkuwachiritsa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:22 Yesaya 1, ptsa. 205-206
22 Yehova adzalanga Iguputo.+ Adzamulanga kenako nʼkumuchiritsa. Iwo adzabwerera kwa Yehova ndipo iye adzamva kuchonderera kwawo nʼkuwachiritsa.