Yesaya 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakantha Iguputo.+ Adzamukantha n’kumuchiza,+ ndipo iwo adzabwerera kwa Yehova.+ Iye adzamva kuchonderera kwawo ndipo adzawachiritsa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:22 Yesaya 1, ptsa. 205-206
22 Yehova adzakantha Iguputo.+ Adzamukantha n’kumuchiza,+ ndipo iwo adzabwerera kwa Yehova.+ Iye adzamva kuchonderera kwawo ndipo adzawachiritsa.+