Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+

      Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+

      Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+

      Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+

      Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+

  • Yesaya 57:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ine ndaona njira zake. Ndinayamba kumuchiritsa+ ndi kumutsogolera,+ ndiponso ndinamutonthoza+ iyeyo ndi anthu ake amene anali kulira.”+

  • Yeremiya 33:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye wanena kuti: ‘Ine ndichiritsa anthu a mumzindawu ndi kuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa ndi kuwapatsa mtendere wochuluka ndi choonadi.+

  • Hoseya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Bwerani anthu inu. Tiyeni tibwerere kwa Yehova,+ pakuti iye watikhadzulakhadzula+ koma adzatichiritsa.+ Wakhala akutivulaza koma adzamanga zilonda zathu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena