Yesaya 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’tsiku limenelo, padzakhala mizinda isanu m’dziko la Iguputo+ yolankhula chinenero cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira+ kwa Yehova wa makamu. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko. Yeremiya 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:
18 M’tsiku limenelo, padzakhala mizinda isanu m’dziko la Iguputo+ yolankhula chinenero cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira+ kwa Yehova wa makamu. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko.
44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti: