Yesaya 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uwu ndi uthenga wokhudza Duma:* Ndikumva winawake akundifunsa mofuula kuchokera ku Seiri kuti:+ “Mlonda, kodi kwatsala nthawi yaitali bwanji kuti kuche? Mlonda, kodi kwatsala nthawi yaitali bwanji kuti kuche?” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:11 Yesaya 1, ptsa. 225, 227
11 Uwu ndi uthenga wokhudza Duma:* Ndikumva winawake akundifunsa mofuula kuchokera ku Seiri kuti:+ “Mlonda, kodi kwatsala nthawi yaitali bwanji kuti kuche? Mlonda, kodi kwatsala nthawi yaitali bwanji kuti kuche?”