Yesaya 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uwu ndi uthenga wokhudza Duma: Ndikumva winawake akundifunsa mofuula kuchokera ku Seiri+ kuti: “Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji? Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji?”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:11 Yesaya 1, ptsa. 225, 227
11 Uwu ndi uthenga wokhudza Duma: Ndikumva winawake akundifunsa mofuula kuchokera ku Seiri+ kuti: “Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji? Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji?”+