Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+

  • Deuteronomo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+

      “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+

  • Salimo 137:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+

      Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena