Yesaya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu,Inu anthu okhala ku dziko la Tema,+Ndipo mubweretse chakudya kuti mudzapatse munthu amene akuthawa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:14 Yesaya 1, tsa. 228
14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu,Inu anthu okhala ku dziko la Tema,+Ndipo mubweretse chakudya kuti mudzapatse munthu amene akuthawa.