Yesaya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu. Inu anthu okhala ku Tema,+ mukhale ndi chakudya podzakumana ndi munthu amene akuthawa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:14 Yesaya 1, tsa. 228
14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu. Inu anthu okhala ku Tema,+ mukhale ndi chakudya podzakumana ndi munthu amene akuthawa.