Yesaya 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndaleka kumukwiyira.+ Ngati munthu wina ataika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga, Ndidzazipondaponda nʼkuziwotcha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:4 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 22 Yesaya 1, tsa. 286
4 Ndaleka kumukwiyira.+ Ngati munthu wina ataika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga, Ndidzazipondaponda nʼkuziwotcha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye.