Yesaya 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndaleka kumukwiyira.+ Munthu wina akaika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga,+ ndidzazipondaponda ndi kuzitentha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:4 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 22 Yesaya 1, tsa. 286
4 Ndaleka kumukwiyira.+ Munthu wina akaika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga,+ ndidzazipondaponda ndi kuzitentha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye.+