Yesaya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani mwana wa Baladani mfumu ya Babulo, anatumiza makalata ndi mphatso kwa Hezekiya+ chifukwa anamva kuti amadwala ndipo wachira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:1 Mawu a Mulungu, tsa. 118
39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani mwana wa Baladani mfumu ya Babulo, anatumiza makalata ndi mphatso kwa Hezekiya+ chifukwa anamva kuti amadwala ndipo wachira.+