Yesaya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:1 Mawu a Mulungu, tsa. 118
39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+