2 Mafumu 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo, Berodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata+ ndi mphatso kwa Hezekiya chifukwa anamva kuti Hezekiya anali kudwala.
12 Pa nthawi imeneyo, Berodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata+ ndi mphatso kwa Hezekiya chifukwa anamva kuti Hezekiya anali kudwala.